Ndinaona kumaloto ndikutuluka magazi ochuluka ku (nyini yanga) ndipo kunali kofiyila bwino osati kwakuda, ndipo ndine mtsikana wotomeredwa pachinkhoswe chonde yankhani 🖤